@jetu_malawi: PANGOLIN#malawitiktok🇲🇼 #fyp #jetu

Emmu Dee
Emmu Dee
Open In TikTok:
Region: MW
Wednesday 02 July 2025 09:32:04 GMT
951702
38405
1617
1484

Music

Download

Comments

mercy.pemba7
mercy :
koma ine nduopa kumtulutsa pangolin eeeeee titha kumtulutsa anthu 30🤣🤣🤣🤣
2025-07-02 13:26:23
177
timmoh12
Timmoh phiri :
nyimbo iyi Hilco wabeleka nayo ma twins
2025-07-02 16:13:57
288
mwiza160
Mwiza mvina :
palibe Munthu yemwe akunenako kuti mwana ofanana ndi Agogo ake 💘🥰 uyu sangakhale opanda Agogo ake uyu
2025-07-13 23:10:16
1
rfunnyd0207
D1 :
komanso amene amabhakira nyimboyi mumpatse moni😩
2025-07-02 13:28:02
216
user4157067916955
proshine Lee✨💝 :
They can never make me hate Jetu 💖💥
2025-07-02 10:57:10
255
boi4tems
4 GOOD TEMS :
juzi muchapeko pliz😂😂😂
2025-07-02 10:40:54
19
phillo134
Uncle Phillo😎💦 :
jetu unapeza chidzukulu chokuvetsa kukoma💪💪💪💪big up guys
2025-07-02 10:14:31
50
user13506551071281
Kanie babie :
bwinotu Ajetu mavinidwe amenewo mupatsidwa nazo mimba
2025-07-02 13:45:24
62
taccoh0608
Taccoh0608 :
Nduona ngat nyimboyi ajetu muthesa nayo zibwezi za anthu inu ma pangolin akubhampana kuseliku😭😂😂😂
2025-07-03 04:10:13
30
danieltambala550
DAN T :
🔥🔥ine chinachake mwaine chikundizuza kuti ndimange nsalu ndichite nawo nyimboyi
2025-07-02 16:10:48
62
valamanja1
valamanja1 :
Phwanga mulungu azikudalitsa
2025-07-03 09:49:40
14
zunaira.tk
zunaira s Austin Tk :
koma wina ayelekeze kutulusa pangolini waine awonaso 😂😂😂😂
2025-07-02 12:50:34
20
user199439845268
Naomie :
Komatu pangolin m'modzi akutulutsidwa ndi anthu 15 kuseliku😂😂😂😂😂
2025-07-02 13:40:10
36
fatietiwa
tiwa Williams❤️💋🌹 :
I wish nditamutulusa koma eeeeee ndikhoza kusowa nazo ya rent kwinaku😂
2025-07-05 06:23:38
6
cardieb05
khadija abdul :
Nyimbo ndiyomweyi pachigalimoto cha campaign 🥰
2025-07-04 06:30:41
12
aaronmaganga688
Aaron Maganga :
Emmu Dee you're the best manager ever 🔥💪
2025-07-02 12:13:23
80
tamavee1
Tama🐱Vee💜 :
nyimbo yi mmachedwa nayo pati mpaka anzanu pango anathawa nde titulusa chan😭😭😭😭😂😂😂
2025-07-03 18:03:07
18
lingalithu6
Danity🫂💐❤️ :
nyimbo iyi yokha ine ndintulusira peer pressure 😂😂😂kaya sizitha bwino ziwoneka 🤣🤣
2025-07-02 15:35:02
10
miracle18454
miracle :
komatu jetu ka style aka amakakonda 🤣🤣
2025-07-03 16:40:39
15
kelvin89895
kelvin89895 :
jetu my love uyu yekha wina mdzamudula phazi🤣🤣
2025-07-03 06:25:10
10
shallowm8
shallowm :
🔥🔥🔥🔥jetu wathu wathu ♥️
2025-07-02 21:09:43
6
user4696014014872
sue de name👻😍 :
Bola osatulutsa nazo pangolini wa eniake😂😂
2025-07-02 12:44:06
15
linesskalonjere
@Linie K :
yomweyo Jetu☺️😊☺️olo kusamukonda Jetuko munthu ungayambire patipo kkkkk🤣🤣🤣
2025-07-02 15:29:46
26
pa.tie7
PA TIE :
wanga singatuluse ndamuona kale Pena 🤣🤣
2025-07-02 15:34:11
10
harrier13
harrier13 :
Even kudana ndi Jetu ndiyambila pati
2025-07-02 18:33:28
23
To see more videos from user @jetu_malawi, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About