@anniekbm:

Anniek1996🇲🇼🇿🇦
Anniek1996🇲🇼🇿🇦
Open In TikTok:
Region: MW
Sunday 20 July 2025 07:32:45 GMT
239611
9013
1402
2646

Music

Download

Comments

sirjupiter2
Bambo Anu Opeza :
Taziuzedi zitsilu zimenezi maka Maria waku 36💔
2025-07-20 12:01:53
111
chriss.phiri
Chriss Phiri :
ndipo uthengawu ifikire ku galileya ndi ku yudeya
2025-07-21 07:29:16
31
jimmybwanali
jimmybwanali :
Wina wake nkhani iyiyi inamuchitikira mbali yakuno pano ali mbuu anthu angomusinthana ngati mpando wamu minbus 🤣🤣
2025-07-30 14:38:55
0
tammiekanthiti
tammie✨🥀 :
😍😍😍zoonadi mamunanga ndi emweyu wa nkhope ngat akudabwayu
2025-07-21 05:18:29
57
eveyreen.somanje2
Eveyreen somanje2 :
ife akungosowa koma zibwana ndilibe
2025-07-22 20:59:55
14
ajeli.mw
Ajeli Yao Boy 🇲🇼🇿🇦 :
tapanga ya amuna ozinva u handsome wa amaona ngt mkaz aliyense ndi wawo 😌
2025-07-21 05:30:27
18
pagone33
Abdrazaq Isaac Pagone :
Bola uziyankhula zomwe umapanga
2025-07-23 10:09:52
5
fauziya897
FAUZIYA :
malangizo abwino mulungu azikupasani zosowa zanu🙏
2025-07-22 10:10:55
16
haluedwilson
Zachmkoz :
Good advice 🥀
2025-07-23 19:09:24
1
frankjustice04
frankjustice04 :
Ife kwinako timapitilako kukathesa kuzigomela kuja😂😂😂
2025-07-21 08:41:09
6
cenation73
cenation73 :
ndiye wati umwa chani? 🥛
2025-07-20 18:16:43
11
josophatlinde763
josophatlinde763 :
ukhale ndimoyo wautali aisee💥👍
2025-07-21 10:42:51
20
antambalika
Ntamba :
Tell them the truth
2025-07-23 17:12:10
3
user9487251509530
user9487251509530 :
adona nyengo zinasintha pano timagowasiya basi tioneso wina
2025-07-21 10:52:41
9
burtongalula
Cool bouy :
kuyankhula ndiye uku ☺️🥰🥰
2025-07-21 09:13:12
5
abdul.ziyade
Abdul Ziyade :
Sister Kodi muli kutiko ndikuponyeleni inayake 💪 this is powerful massage 💃💃
2025-07-21 12:56:42
7
maloni.alufeyo1
Maloni Alufeyo :
A mayi mulindi zeru a ambuye akudalitseni.
2025-07-21 03:20:35
16
gracekamanga4
Grace :
Nzeru mama
2025-07-21 10:10:53
18
kaliyekha
wiseman :
Odi ndikupange follow ine good advice cc🙏
2025-07-20 19:33:40
3
prophetinnoangelo
Promise Thengoliweta :
mkazi koma uyuu landila ulemu wako ukanali moyoo asee🎉🎉🎉
2025-07-20 19:08:52
15
dorice3042
Dorice :
zikomo kwambili dear
2025-07-20 12:27:46
6
user5110205834033
precious Banda :
takumananawo ife chiserekwete cha nkazi ndithu pamalangizo anu mama pitilizani mwina ena asitha
2025-07-24 07:27:36
3
isaacnayes
Isaac :
muli pa banja kale ??????
2025-07-27 05:35:14
2
vasco_vee_nkhoma
Vasco_Vee_Nkhoma :
Mkazi wa nzeru
2025-07-20 14:38:03
10
1911ben71
Bentry Phiri :
Kodi mmakhala kuti mukuwelenga Kapena you speak from the heart?
2025-07-22 08:32:14
8
To see more videos from user @anniekbm, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About