the blood of innocent souls from chikangawa troubling their souls
2025-10-07 03:01:17
5
BeiRo :
as a patriotic citizen ineyo it pains me seeing Publc infrustructure being vandalized like that.....i have been to Bingu stadium, ma toilet, zitseko etc kuononga aaaa abalee we can do better than that abale
2025-10-07 07:06:03
0
Mercy :
koma chakwera ku ubusa akangobisalako apa ndiye wayaluka🤣🤣
2025-10-07 18:00:34
0
Rosemary Chimbiya :
wonse anali kumeneko amangidwe upandu umenewo
2025-10-07 17:19:57
2
BOSSLADY :
nnaziwa ine kuti agalu awa anyelako amakakamilila zomwezo
2025-10-07 17:52:36
0
Dr.Yakobe MBEWE :
umanyerako ndi iweyo ndiwe chitsiru wopanda nzeru ndi Chakwera wakoyo
2025-10-08 14:18:52
0
kettie Hassan :
Chakwera ndi MCP awononga state house
mu mbiri ya Malawi a chakwera ndi amene awononga kwambiri kwambiri mmmmm shame shame
2025-10-08 13:36:59
0
To see more videos from user @big.yao55, please go to the Tikwm
homepage.