@ackimsaini: Malemu Maxwell Chinomwe ati anakondwa kwambiri Sunday pa 9 November pamene Captain wa Silver Maxwell Paipi anagolesa penalty yomwe inapangisa kuti afanane mphamvu ndi Wanderers pomwe amatsalira 1 kwa 0. Nde atangochinya Maxwell Paipi supporter yu anasangalala kwambiri mpaka kugwa, imfa inali yomweyo. MHSRIP.
Ackim Saini
Region: MW
Tuesday 11 November 2025 15:42:57 GMT
Music
Download
Comments
japhet :
zikomo ambuye pondichotsela chiwanda champila.
2025-11-12 11:59:49
117
carlo :
nkhani sikukondwa kwambiri kma kuti anthufe tsiku lakufa anatibisile mzimu wawo uuse mumtendere bambo a Zaithwa 😥😥😥😥😥
2025-11-12 11:36:25
199
hassie :
ine zampirazi nnasiya
2025-11-19 18:28:33
0
ULLITER🌹❤️🔥 :
. Mmmmmm zosayenda tu abale kodi zinali zoonadi 😭😭😭😭😭😭
2025-11-13 06:29:57
0
Destiny :
nde achipatala anapanga confirm Kut chamupha ndikukodwako🥹
2025-11-13 10:19:21
11
Thandiwe Mvula :
mesa akuti anapanga ngozi anthuwa kodi
2025-11-12 11:51:34
5
Thandi_aggie :
moyowu Kodi ndi otani? ukakhumudwa umafa ukakondwa umafa basi titani kweni kweni Ambuye? 😭😭😭😭😭😭
2025-11-12 12:04:34
72
Maureen Kambiya😍😍 :
kodi kunali kukondwa osati ngodzi?
2025-11-12 14:25:10
5
NettieKay :
Zovutatu kunvetsetsa
2025-11-12 11:47:47
1
Angie🦋💟 :
Eeh eeh tisakondwenso kwambiri tizifa!🥺
2025-11-12 11:15:57
21
Super chick😍😍 :
koma Manoma 🥹
2025-11-12 12:35:06
5
user6575315709650 :
zosayenda😭😭😭 aliyese wakewake ulendo mulungu anatibisira chisisi
2025-11-13 12:53:00
3
0996420405 :
nthawi yake inangokwana😅
2025-11-13 10:54:19
1
Patricia :
Inachitikanso ku nambuma abambo ena ake anali a police tram yao itagoletsa anakuea badi imfanso inali yomeeyo😭😭😭😭
2025-11-13 18:43:26
2
Antony1995 :
Kuutengela pa mgong'o tu mpira
2025-11-12 16:35:43
1
philbet20 :
FDH cup yomweyi kkkkkkk
2025-11-13 10:55:18
1
Chichi ❣️❣️ :
RPC 😭😭😭
2025-11-14 10:49:12
0
memory :
zosayenda koma 😭
2025-11-13 16:16:42
1
Shamim Kazembe :
ummmm kodi kukondwaso nkulakwa?🤔
2025-11-13 08:21:44
1
Elina Nkuta :
kukondwa kwambili? mpaka kufa ?eeeh eeh moyowutu
2025-11-12 13:48:52
1
Tinkie2001 :
Ukakondwa mmm wambiri nsempha wamubongo umafufuma abd can burst 🙌🏽
2025-11-12 12:52:08
8
user4456210545503 :
kod zamoyo zmakhala bwanj tisakondwens
2025-11-13 09:48:26
1
Teleza Msamala :
ndichifukwa ndilibe team 🙏
2025-11-13 12:52:29
1
Mary Banda :
mwati chinamupha chani abale
2025-11-13 19:57:23
1
nkosiyaziminandi :
Game imeneyi ndiye kuti yapha anthu awili. very sad
2025-11-13 16:03:09
1
To see more videos from user @ackimsaini, please go to the Tikwm
homepage.